-
Takulandirani ku
TheocBase
TheocBase ndi chida cha Mboni za Yehova Chokonzera Misonkhano ya Mkati mwa Mlungu ndi Lamlungu
Mungapereke chinthu chilichonse chphunzira pamsonkhanowu chomwe chinachokera ku buku la moyo wathu komanso / kapena WT (epub-format)
Imathandizanso Woyang'anila Utumiki ndi Moyo wathu Wachikhistu kuti atsatile ntchito za ophunzira
-
Kuyambapo
Choyamba lowetsani zofunikira monga mpingo wanu komanso nthawi zoyambira misonkhano
Chotsatira: Lowetsani Maina a anthu ndi Kuwagawira Mbali zomwe angapatsidwe.
Kenaka lowetsani zofunika monga maphunziro kapena nkhani zaonse muTheocBase
-
Ndandani Zinthu Zamsonkhano
Lowetsani ndondomeko ya Msonkhano kudzera pa epub kapena lowetsani pamanja.
Pazithunzi zazikulu patsani abale mapologalamu osiyanasiyana ndi / kapena mukonze Nkhani za onse (Wobwera ndi Wotuluka).
Gwiritsani ntchito zosiyana pamakonzedwe kuti musamalire zochitika zapadera monga maulendo a woyang'anira dera
-
Sungani ntchito za ophunzira
Onetsetsani zotsatira za phunziro / ntchito yotsirizidwa ndi kulemba Mfundo pa tsamba lalikulu
Mukhozanso kusintha mbiri yakale ya wophunzira pamanja
-
Zochitika Zotsogola
Kufananitsa ndi pachipangizo| Kusunga ndi Kubwezeretsa
Mogwirizana ndi app TheocBase mafoni mungathe kusinthanitsa zonse za mmbuyo.
Njira ina ndi kuitanitsa / kutumizira uthenga ndikukutumiza kudzera pa imelo.